Agoloso Presents - Atondido Stories Agoloso Presents - Paphata pa Chichewa | Page 80

Paphata pa Chichewa (b) Ana akulephera mayeso chifukwa chojomba kusukulu. Judula: (a) Kukonza chinthu kuti chioneke bwino kwambiri. Chitsanzo: Njingayi ndikaijudula simuidziwa. (b) Kubera munthu kapena kumupusitsa. Chitsanzo: Madobadoba a m’tauni amujudula ndalama zake. (c) Kudzikongoletsa. Chitsanzo: Koma ndiye mwadzijudulatu! 79