Agoloso Presents - Atondido Stories Agoloso Presents - Paphata pa Chichewa | Page 78

Paphata pa Chichewa Ithwa pakamwa: Kukhala munthu wodziwa kuyankhula, kuyankhula mosabisa mawu, kuyankhula bwino. Chitsanzo: Kumsika kumafuna anthu akuthwa pakamwa. Iwala gaga (siya gaga): Mawu achipongwe onena za munthu amene wamwalira. Chitsanzo: (1) Chigawenga chija chinasiya gaga. (2) Osamakonda kusewera pansewu mungasiye gaga. (3) Nkhalamo ija inaiwala gaga. 77