Agoloso Presents - Atondido Stories Agoloso Presents - Paphata pa Chichewa | Page 73

Paphata pa Chichewa Gwirira m’chisa: Dzidzimutsa. Chitsanzo: Ndinakana ulendowo chifukwa anandigwirira m’chisa. Gwiritsa fuwa lamoto: Kupusitsa kapena kudikiriritsana popanda kanthu. Chitsanzo: Amakonda kugwiritsa anzake fuwa lamoto. Gwiritsa: Osapusa chifukwa ena akhoza kukulanda. Chitsanzo: Amuna anuwa muwagwiritse, anzanu maso ali pomwepa. 72