Agoloso Presents - Atondido Stories Agoloso Presents - Paphata pa Chichewa | Page 316

Paphata pa Chichewa Osati masewera: Kwambiri. Chitsanzo: Mwana wanu aphunzitsi amumenya osati masewera. Otaika: Osokonekera. Chitsanzo: Ana awo onse ndi otaika. Othyasika: Ochenjeretsa, Olongolola. Chitanzo: Atsikana ake ndi othyasika. Otolatola: Akuba. Chitsanzo: Ana awo onse ndi otolatola. Ovololo: Chovala chomwe ukhoza kuchivala kuyambira kumiyendo mpaka kumutu. Chisanzo: Bambo avala ovololo. 315