Agoloso Presents - Atondido Stories Agoloso Presents - Miyambi ya Patsokwe | Page 67

Miyambi ya Patsokwe Inswa ikaola imodzi, zaola zonse. -Pamudzi munthu akakhala wamakhalidwe oipa monga waku- ba, anthu amangoti mudzi wonse ndi wa anthu akuba ngakhale wakuba ali mā€™modzi yekha. Kulakwa kwa munthu wina kukho- za kukhudza anthu ena. 66