Agoloso Presents - Atondido Stories Agoloso Presents - Miyambi ya Patsokwe | Page 265

Miyambi ya Patsokwe Woyenga mafuta satuwa. -Munthu amapeza zimene akufunikira pamene amagwira ntchi- to. Woyerekedwa anagwa m’mpheto mwa apongozi. -Munthu ukamachita zinthu moyerekedwa, nthawi zina umadzachita zinthu zosayenera monga kugwera apongozi pov- ina. 264