Agoloso Presents - Atondido Stories Agoloso Presents - Matigari | Page 55

Matigari m’mutu mwake. Anthu ena aja anabalalikira mbali zosiyanasiyana akukambi- rana zomwe zinachitikazo. Iwo ankauza aliyense za apolisi aja, galu, komanso za Guthera ndi Matigari. Ena ankafunsana kuti: “Kodi Matigari ndi ndani?” 54