Agoloso Presents - Atondido Stories Agoloso Presents - Matigari | Page 248

Matigari Kodi Matigari ndi mpulumutsi kapena wamisala? Kodi ndi munthu wamwamuna kapena wamkazi? Kodi ndi mwana kapena munthu wamkulu? Kapena anali m'maganizo mwa an- thu basi, chifaniziro chomwe chinkayendayenda m'maganizo mwa anthu? Ko d i Matigari nd i nd ani k wenik weni? 247